-
Machitidwe 23:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Atatero, Paulo anamuuza kuti: “Uona, Mulungu akulanga, khoma lopaka laimu iwe. Wakhala pamenepo kuti undiweruze motsatira Chilamulo, ndiye ukuphwanyanso Chilamulocho polamula kuti andimenye?”
-