-
Machitidwe 23:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Tsopano inuyo ndi Khoti Lalikulu la Ayuda, muuze mkulu wa asilikali kuti abweretse Paulo kwa inu ngati kuti mukufuna kumvetsa bwino nkhani yake. Koma asanafike ife tidzamupha.”
-