-
Machitidwe 23:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho Paulo anaitana mmodzi wa atsogoleri a asilikali nʼkumuuza kuti: “Mʼtenge mnyamatayu upite naye kwa mkulu wa asilikali chifukwa ali ndi mawu oti akamuuze.”
-