-
Machitidwe 23:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho anamutengadi nʼkupita naye kwa mkulu wa asilikali ndipo ananena kuti: “Paulo, mkaidi uja, anandiitana nʼkundiuza kuti ndimubweretse mnyamatayu. Akuti ali ndi mawu oti akuuzeni.”
-