Machitidwe 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anati: “Ayuda agwirizana zoti akupempheni kuti mawa mupititse Paulo kubwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda, ngati kuti akufuna kumvetsa bwino mlandu wake.+
20 Iye anati: “Ayuda agwirizana zoti akupempheni kuti mawa mupititse Paulo kubwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda, ngati kuti akufuna kumvetsa bwino mlandu wake.+