Machitidwe 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno anaitanitsa atsogoleri awiri a asilikali nʼkuwauza kuti: “Uzani asilikali 200 kuti akonzekere kuyenda ulendo wopita ku Kaisareya cha mʼma 9 koloko* usiku uno. Pakhalenso amuna 70 okwera pamahatchi* ndiponso asilikali 200 a mikondo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:23 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 191
23 Ndiyeno anaitanitsa atsogoleri awiri a asilikali nʼkuwauza kuti: “Uzani asilikali 200 kuti akonzekere kuyenda ulendo wopita ku Kaisareya cha mʼma 9 koloko* usiku uno. Pakhalenso amuna 70 okwera pamahatchi* ndiponso asilikali 200 a mikondo.