Machitidwe 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu uyu anagwidwa ndi Ayuda ndipo anatsala pangʼono kumupha. Koma nthawi yomweyo ndinafika ndi gulu langa la asilikali nʼkumupulumutsa,+ chifukwa ndinamva kuti iyeyu ndi nzika ya Roma.+
27 Munthu uyu anagwidwa ndi Ayuda ndipo anatsala pangʼono kumupha. Koma nthawi yomweyo ndinafika ndi gulu langa la asilikali nʼkumupulumutsa,+ chifukwa ndinamva kuti iyeyu ndi nzika ya Roma.+