Machitidwe 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno pofuna kudziwa chimene anapalamula, ndinapita naye ku Khoti Lalikulu la Ayuda.+