Machitidwe 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera kuphedwa kapena kutsekeredwa mʼndende.
29 Kumeneko ndinapeza kuti akumuimba mlandu pa nkhani zokhudza Chilamulo chawo.+ Koma sanapezeke ndi mlandu uliwonse woyenera kuphedwa kapena kutsekeredwa mʼndende.