Machitidwe 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Komabe popeza ndadziwa chiwembu chimene amukonzera munthuyu,+ ndamutumiza kwa inu, ndipo ndalamula omuimba mlanduwo kuti adzanene mlandu wake pamaso panu.”
30 Komabe popeza ndadziwa chiwembu chimene amukonzera munthuyu,+ ndamutumiza kwa inu, ndipo ndalamula omuimba mlanduwo kuti adzanene mlandu wake pamaso panu.”