Machitidwe 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho asilikaliwo anatenga Paulo+ usiku nʼkupita naye ku Antipatiri mogwirizana ndi zimene anawalamula.
31 Choncho asilikaliwo anatenga Paulo+ usiku nʼkupita naye ku Antipatiri mogwirizana ndi zimene anawalamula.