-
Machitidwe 23:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Tsiku lotsatira anasiya amuna okwera pamahatchi aja kuti apitirire naye, koma iwo anabwerera kumpanda wa asilikali.
-