Machitidwe 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno anati: “Ndimvetsera mlandu wako wonse anthu okuimba mlanduwo akafika.”+ Ndipo analamula kuti amusunge mʼnyumba ya Mfumu Herode nʼkumamulondera.
35 Ndiyeno anati: “Ndimvetsera mlandu wako wonse anthu okuimba mlanduwo akafika.”+ Ndipo analamula kuti amusunge mʼnyumba ya Mfumu Herode nʼkumamulondera.