-
Machitidwe 24:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Teritulo atapatsidwa mwayi kuti alankhule, anayamba kumuneneza Paulo kuti:
“Tili pa mtendere wambiri chifukwa cha inu, komanso zinthu zikusintha mu mtundu wathuwu chifukwa cha nzeru zanu zoona patali.
-