Machitidwe 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda padziko lonse. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko la anthu a ku Nazareti.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:5 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 192 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, ptsa. 22-23
5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda padziko lonse. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko la anthu a ku Nazareti.+