Machitidwe 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Bwanamkubwayo atagwedezera Paulo mutu kuti alankhule, Paulo anayankha kuti: “Ndikudziwa kuti mwakhala woweruza wa mtundu uwu kwa zaka zambiri. Choncho ndine wosangalala kulankhula podziteteza pa zimene akundinenerazi.+
10 Bwanamkubwayo atagwedezera Paulo mutu kuti alankhule, Paulo anayankha kuti: “Ndikudziwa kuti mwakhala woweruza wa mtundu uwu kwa zaka zambiri. Choncho ndine wosangalala kulankhula podziteteza pa zimene akundinenerazi.+