-
Machitidwe 24:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndipo iwowa sanandipezepo mʼkachisi ndikutsutsana ndi aliyense. Sanandipezenso ndikuyambitsa chipolowe mʼmasunagoge kapena pena paliponse mumzindawu.
-