Machitidwe 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa cha zimenezi, ndikuyesetsa mwakhama kuti ndikhale ndi chikumbumtima chabwino kwa Mulungu ndiponso kwa anthu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:16 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, ptsa. 14-15
16 Chifukwa cha zimenezi, ndikuyesetsa mwakhama kuti ndikhale ndi chikumbumtima chabwino kwa Mulungu ndiponso kwa anthu.+