Machitidwe 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mawu amodzi okha amene ine ndinanena, pamene ndinaima pakati pawo ndi akuti, ‘Ine lero ndikuweruzidwa chifukwa cha chiyembekezo chakuti akufa adzauka!’”+
21 Mawu amodzi okha amene ine ndinanena, pamene ndinaima pakati pawo ndi akuti, ‘Ine lero ndikuweruzidwa chifukwa cha chiyembekezo chakuti akufa adzauka!’”+