Machitidwe 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pamene ankafotokoza zokhudza chilungamo, kudziletsa ndiponso chiweruzo chimene chikubwera,+ Felike anachita mantha ndipo anati: “Basi pita kaye, ndikadzapeza nthawi ndidzakuitananso.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:25 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 194-195 Nsanja ya Olonda,8/15/1993, ptsa. 17-19
25 Koma pamene ankafotokoza zokhudza chilungamo, kudziletsa ndiponso chiweruzo chimene chikubwera,+ Felike anachita mantha ndipo anati: “Basi pita kaye, ndikadzapeza nthawi ndidzakuitananso.”