Machitidwe 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Patatha zaka ziwiri, Felike analowedwa mʼmalo ndi Porikiyo Fesito. Koma popeza Felike ankafuna kuti Ayuda azimukonda,+ anangomusiya Paulo mʼndende. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:27 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 195
27 Patatha zaka ziwiri, Felike analowedwa mʼmalo ndi Porikiyo Fesito. Koma popeza Felike ankafuna kuti Ayuda azimukonda,+ anangomusiya Paulo mʼndende.