Machitidwe 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Patatha masiku atatu kuchokera pamene Fesito+ anafika mʼchigawocho nʼkuyamba kulamulira, anapita ku Yerusalemu kuchokera ku Kaisareya. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:1 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 196
25 Patatha masiku atatu kuchokera pamene Fesito+ anafika mʼchigawocho nʼkuyamba kulamulira, anapita ku Yerusalemu kuchokera ku Kaisareya.