Machitidwe 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anati: “Amene ali ndi maudindo pakati panu, tipitire limodzi kuti ngati pali chilichonse chimene munthu ameneyu walakwa akamuimbe mlandu.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:5 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 196
5 Ndiyeno anati: “Amene ali ndi maudindo pakati panu, tipitire limodzi kuti ngati pali chilichonse chimene munthu ameneyu walakwa akamuimbe mlandu.”+