-
Machitidwe 25:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho iye atakhala nawo kumeneko kwa masiku osapitirira 8 kapena 10, anabwerera ku Kaisareya. Ndipo tsiku lotsatira anakhala pampando woweruzira milandu nʼkuuza anthu kuti abweretse Paulo.
-