Machitidwe 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Paulo atafika, Ayuda amene anabwera kuchokera ku Yerusalemu, anaima momuzungulira nʼkumamuneneza milandu yambiri yoopsa, imene sanathe kupereka umboni wake.+
7 Paulo atafika, Ayuda amene anabwera kuchokera ku Yerusalemu, anaima momuzungulira nʼkumamuneneza milandu yambiri yoopsa, imene sanathe kupereka umboni wake.+