Machitidwe 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Paulo podziteteza anati: “Ine sindinachimwire Chilamulo cha Ayuda kapena kachisi kapenanso Kaisara.”+
8 Koma Paulo podziteteza anati: “Ine sindinachimwire Chilamulo cha Ayuda kapena kachisi kapenanso Kaisara.”+