Machitidwe 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma pofuna kuti Ayudawo amukonde,+ Fesito anafunsa Paulo kuti: “Kodi ukufuna kupita ku Yerusalemu kuti nkhaniyi ikaweruzidwe kumeneko pamaso panga?” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:9 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 197-198 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, ptsa. 23-24
9 Koma pofuna kuti Ayudawo amukonde,+ Fesito anafunsa Paulo kuti: “Kodi ukufuna kupita ku Yerusalemu kuti nkhaniyi ikaweruzidwe kumeneko pamaso panga?”