-
Machitidwe 25:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma Paulo anayankha kuti: “Ine ndaima kutsogolo kwa mpando woweruzira milandu wa Kaisara, kumene ndiyenera kuweruzidwa. Ayuda sindinawalakwire chilichonse ngati mmene inunso mukuonera.
-