-
Machitidwe 25:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Patatha masiku angapo, Mfumu Agiripa ndi Berenike anafika ku Kaisareya pa ulendo wa boma wokapereka ulemu kwa Fesito.
-