-
Machitidwe 25:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Popeza anakhala kumeneko masiku angapo, Fesito anafotokozera mfumuyo nkhani yokhudza Paulo. Iye anati:
“Pali munthu wina amene Felike anamusiya mʼndende.
-