Machitidwe 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamene ndinali ku Yerusalemu, ansembe aakulu komanso akulu a Ayuda anabwera kudzandiuza zoipa zokhudza iyeyu+ ndipo anapempha chiweruzo choti aphedwe.
15 Pamene ndinali ku Yerusalemu, ansembe aakulu komanso akulu a Ayuda anabwera kudzandiuza zoipa zokhudza iyeyu+ ndipo anapempha chiweruzo choti aphedwe.