Machitidwe 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine ndinawayankha kuti Aroma sachita zinthu mʼnjira imeneyo. Iwo sapereka munthu kwa anthu omuneneza pongofuna kuwasangalatsa, munthu wonenezedwayo asanapatsidwe mwayi woonana pamasomʼpamaso ndi omunenezawo kuti adziteteze pa mlanduwo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:16 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, tsa. 23
16 Koma ine ndinawayankha kuti Aroma sachita zinthu mʼnjira imeneyo. Iwo sapereka munthu kwa anthu omuneneza pongofuna kuwasangalatsa, munthu wonenezedwayo asanapatsidwe mwayi woonana pamasomʼpamaso ndi omunenezawo kuti adziteteze pa mlanduwo.+