Machitidwe 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo ankangotsutsana naye nkhani zokhudza mmene amalambirira mulungu*+ komanso za munthu wina dzina lake Yesu amene anafa, koma Paulo akunenabe motsimikiza kuti ali moyo.+
19 Iwo ankangotsutsana naye nkhani zokhudza mmene amalambirira mulungu*+ komanso za munthu wina dzina lake Yesu amene anafa, koma Paulo akunenabe motsimikiza kuti ali moyo.+