Machitidwe 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nditalephera kuthetsa mkangano wa nkhani zimenezi, ndinamufunsa ngati akufuna kupita ku Yerusalemu kuti akaweruzidwe kumeneko.+
20 Nditalephera kuthetsa mkangano wa nkhani zimenezi, ndinamufunsa ngati akufuna kupita ku Yerusalemu kuti akaweruzidwe kumeneko.+