Machitidwe 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Agiripa anauza Fesito kuti: “Inenso ndikufuna ndimve ndekha munthu ameneyu akulankhula.”+ Iye anati: “Mawa mudzamumvetsera.”
22 Agiripa anauza Fesito kuti: “Inenso ndikufuna ndimve ndekha munthu ameneyu akulankhula.”+ Iye anati: “Mawa mudzamumvetsera.”