Machitidwe 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Fesito ananena kuti: “Mfumu Agiripa ndi anthu nonse amene muli nafe pano, mwamuona munthuyu? Ayuda onse ku Yerusalemu komanso kuno, anandipempha kuti iyeyu sakuyeneranso kukhala ndi moyo ndipo analankhula zimenezi mofuula.+
24 Ndiyeno Fesito ananena kuti: “Mfumu Agiripa ndi anthu nonse amene muli nafe pano, mwamuona munthuyu? Ayuda onse ku Yerusalemu komanso kuno, anandipempha kuti iyeyu sakuyeneranso kukhala ndi moyo ndipo analankhula zimenezi mofuula.+