-
Machitidwe 25:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Koma ndilibe mfundo iliyonse imene ndingalembere Mbuyanga yokhudza munthuyu. Choncho ndamubweretsa kwa nonsenu, makamaka inu Mfumu Agiripa, kuti mukamufunsa za nkhaniyi, ndipeze cholemba.
-