Machitidwe 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Agiripa+ anauza Paulo kuti: “Ukhoza kulankhula mbali yako.” Ndiyeno Paulo anakweza dzanja nʼkuyamba kulankhula modziteteza kuti:
26 Agiripa+ anauza Paulo kuti: “Ukhoza kulankhula mbali yako.” Ndiyeno Paulo anakweza dzanja nʼkuyamba kulankhula modziteteza kuti: