-
Machitidwe 26:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Makamaka chifukwa chakuti ndinu katswiri pa miyambo yonse komanso pa zimene Ayuda amakangana. Choncho ndikukupemphani kuti mundimvetsere moleza mtima.
-