-
Machitidwe 26:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Nthawi zambiri ndinkawapatsa chilango mʼmasunagoge onse, pofuna kuwakakamiza kuti asiye zimene amakhulupirira. Popeza ndinali nditakwiya nawo kwambiri, ndinafika powazunza ngakhale mʼmizinda yakunja.
-