Machitidwe 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ndili mʼnjira dzuwa lili pamutu, inu mfumu, ndinaona kuwala kochokera kumwamba koposa kuwala kwa dzuwa ndipo kunandizungulira ineyo ndiponso anthu amene ndinali nawo pa ulendowu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:13 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 200
13 Koma ndili mʼnjira dzuwa lili pamutu, inu mfumu, ndinaona kuwala kochokera kumwamba koposa kuwala kwa dzuwa ndipo kunandizungulira ineyo ndiponso anthu amene ndinali nawo pa ulendowu.+