-
Machitidwe 26:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Pamene Paulo ankanena zimenezi podziteteza, Fesito ananena mokweza mawu kuti: “Wachita misala iwe Paulo! Kuphunzira kwambiri kwakupengetsa!”
-