Machitidwe 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kunena zoona, ndikulankhula momasuka chifukwa mfumu imene ndikulankhula nayo ikudziwa bwino zimenezi. Sindikukayikira kuti palibe ngakhale chimodzi mwa zinthu zimenezi, chimene simukuchidziwa chifukwa zimenezi sizinachitike mwamseri.+
26 Kunena zoona, ndikulankhula momasuka chifukwa mfumu imene ndikulankhula nayo ikudziwa bwino zimenezi. Sindikukayikira kuti palibe ngakhale chimodzi mwa zinthu zimenezi, chimene simukuchidziwa chifukwa zimenezi sizinachitike mwamseri.+