-
Machitidwe 26:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ndiyeno Paulo anati: “Kaya pa nthawi yochepa kapena yaitali, pemphero langa kwa Mulungu ndi lakuti, onse amene andimvetsera lero, osati inu nokha, akhale ngati ine kupatulapo maunyolo okhawa.”
-