Machitidwe 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ulendo wathu wapamadzi wopita ku Italy+ utatsimikizika, Paulo ndi akaidi ena anaperekedwa mʼmanja mwa mtsogoleri wa asilikali dzina lake Yuliyo, wamʼgulu la asilikali la Augusito.
27 Ulendo wathu wapamadzi wopita ku Italy+ utatsimikizika, Paulo ndi akaidi ena anaperekedwa mʼmanja mwa mtsogoleri wa asilikali dzina lake Yuliyo, wamʼgulu la asilikali la Augusito.