-
Machitidwe 27:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Titalowanso panyanja kuchokera kumeneko, tinayenda mʼmbali mwa chilumba cha Kupuro chimene chinkatiteteza ku mphepo imene inkawomba kuchokera kumene ife tinkapita.
-