Machitidwe 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano panali patapita nthawi yaitali, ndipo kuyenda panyanja kunali koopsa chifukwa ngakhale nthawi ya kusala kudya kwa Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo+ inali itadutsa kale. Choncho Paulo anawapatsa malangizo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:9 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 205-207 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2017, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,2/1/2010, tsa. 233/15/1999, tsa. 31
9 Tsopano panali patapita nthawi yaitali, ndipo kuyenda panyanja kunali koopsa chifukwa ngakhale nthawi ya kusala kudya kwa Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo+ inali itadutsa kale. Choncho Paulo anawapatsa malangizo.
27:9 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 205-207 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2017, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,2/1/2010, tsa. 233/15/1999, tsa. 31