-
Machitidwe 27:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma mtsogoleri wa asilikali anamvera woyendetsa ngalawa ndi mwiniwake wa ngalawayo mʼmalo momvera zimene Paulo ananena.
-