-
Machitidwe 27:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Popeza dokolo silinali labwino kukhalapo nthawi yozizira, anthu ambiri anagwirizana ndi zoti achokepo. Iwo ankafuna kuona ngati nʼzotheka kukafika ku Finikesi kuti akakhale kumeneko nthawi yozizira. Finikesi linali doko la Kerete loyangʼana kumpoto chakumʼmawa ndi kumʼmwera chakumʼmawa.
-