-
Machitidwe 27:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mphepo yakumʼmwera itayamba kuwomba pangʼonopangʼono, anaganiza kuti zimene ankafuna zitheka. Choncho anakweza nangula nʼkuyamba kuyenda mʼmbali mwa chilumba cha Kerete.
-